Quran with Chichewa translation - Surah As-saffat ayat 148 - الصَّافَات - Page - Juz 23
﴿فَـَٔامَنُواْ فَمَتَّعۡنَٰهُمۡ إِلَىٰ حِينٖ ﴾
[الصَّافَات: 148]
﴿فآمنوا فمتعناهم إلى حين﴾ [الصَّافَات: 148]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo adakhulupirira (ndi kuvomereza ulaliki wake); choncho tidawapatsa chisangalalo kufikira nthawi (ya imfa yawo) |