Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 11 - الزُّمَر - Page - Juz 23
﴿قُلۡ إِنِّيٓ أُمِرۡتُ أَنۡ أَعۡبُدَ ٱللَّهَ مُخۡلِصٗا لَّهُ ٱلدِّينَ ﴾
[الزُّمَر: 11]
﴿قل إني أمرت أن أعبد الله مخلصا له الدين﴾ [الزُّمَر: 11]
Khaled Ibrahim Betala “Nena: “Ine ndalamulidwa kuti ndimpembedze Allah momuyeretsera mapemphero Ake (posamphatikiza ndi aliyense pa mapemphero, kapena kupemphera mwa chiphamaso).” |