×

Ndipo pamene dzina la Mulungu lokha litchulidwa, mitima ya iwo amene sakhulupirira 39:45 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:45) ayat 45 in Chichewa

39:45 Surah Az-Zumar ayat 45 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 45 - الزُّمَر - Page - Juz 24

﴿وَإِذَا ذُكِرَ ٱللَّهُ وَحۡدَهُ ٱشۡمَأَزَّتۡ قُلُوبُ ٱلَّذِينَ لَا يُؤۡمِنُونَ بِٱلۡأٓخِرَةِۖ وَإِذَا ذُكِرَ ٱلَّذِينَ مِن دُونِهِۦٓ إِذَا هُمۡ يَسۡتَبۡشِرُونَ ﴾
[الزُّمَر: 45]

Ndipo pamene dzina la Mulungu lokha litchulidwa, mitima ya iwo amene sakhulupirira za m’moyo umene uli nkudza imakhumudwa koma pamene milungu ina kupatula Mulungu weniweni itchulidwa, iwo amasangalala kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا ذكر الله وحده اشمأزت قلوب الذين لا يؤمنون بالآخرة وإذا ذكر, باللغة نيانجا

﴿وإذا ذكر الله وحده اشمأزت قلوب الذين لا يؤمنون بالآخرة وإذا ذكر﴾ [الزُّمَر: 45]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo pamene Allah Yekha akutchulidwa, mitima ya amene sakhulupirira tsiku la chimaliziro imanyansidwa; koma akatchulidwa amene sali Iye, iwo amakondwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek