×

Nena “Mphamvu zonse za mkhalapakati zili m’manja mwa Mulungu. Iye ndiye Mwini 39:44 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:44) ayat 44 in Chichewa

39:44 Surah Az-Zumar ayat 44 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 44 - الزُّمَر - Page - Juz 24

﴿قُل لِّلَّهِ ٱلشَّفَٰعَةُ جَمِيعٗاۖ لَّهُۥ مُلۡكُ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِۖ ثُمَّ إِلَيۡهِ تُرۡجَعُونَ ﴾
[الزُّمَر: 44]

Nena “Mphamvu zonse za mkhalapakati zili m’manja mwa Mulungu. Iye ndiye Mwini wa chilichonse chimene chili kumwamba ndi pa dziko lapansi. Ndipo ndi kwa Iye kumene mudzabwerera.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل لله الشفاعة جميعا له ملك السموات والأرض ثم إليه ترجعون, باللغة نيانجا

﴿قل لله الشفاعة جميعا له ملك السموات والأرض ثم إليه ترجعون﴾ [الزُّمَر: 44]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Chiombolo chonse chili kwa Allah; ufumu wa kumwamba ndi pansi Ngwake; kenako kwa Iye m’dzabwezedwa.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek