×

Motero zoipa zimene adachita zidawatsata iwo. Ndipo iwo ochita zoipa a m’badwo 39:51 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:51) ayat 51 in Chichewa

39:51 Surah Az-Zumar ayat 51 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 51 - الزُّمَر - Page - Juz 24

﴿فَأَصَابَهُمۡ سَيِّـَٔاتُ مَا كَسَبُواْۚ وَٱلَّذِينَ ظَلَمُواْ مِنۡ هَٰٓؤُلَآءِ سَيُصِيبُهُمۡ سَيِّـَٔاتُ مَا كَسَبُواْ وَمَا هُم بِمُعۡجِزِينَ ﴾
[الزُّمَر: 51]

Motero zoipa zimene adachita zidawatsata iwo. Ndipo iwo ochita zoipa a m’badwo uno zotsatira za ntchito zawo zidzawapeza ndipo iwo sadzatha kuthawa ayi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فأصابهم سيئات ما كسبوا والذين ظلموا من هؤلاء سيصيبهم سيئات ما كسبوا, باللغة نيانجا

﴿فأصابهم سيئات ما كسبوا والذين ظلموا من هؤلاء سيصيبهم سيئات ما كسبوا﴾ [الزُّمَر: 51]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho, zidawapeza zoipa za zomwe adazichita. Ndipo amene achita chinyengo mwa awa, posachedwa kuwapeza kuipa kwa zomwe achita, ndipo iwo sangamlempheretse (Allah)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek