Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 52 - الزُّمَر - Page - Juz 24
﴿أَوَلَمۡ يَعۡلَمُوٓاْ أَنَّ ٱللَّهَ يَبۡسُطُ ٱلرِّزۡقَ لِمَن يَشَآءُ وَيَقۡدِرُۚ إِنَّ فِي ذَٰلِكَ لَأٓيَٰتٖ لِّقَوۡمٖ يُؤۡمِنُونَ ﴾
[الزُّمَر: 52]
﴿أو لم يعلموا أن الله يبسط الرزق لمن يشاء ويقدر إن في﴾ [الزُّمَر: 52]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi iwo sadziwa kuti Allah amamtambasulira zopatsa zake yemwe wamfuna, ndi kumchepetsera (amene wamfuna)? Ndithu m’zimenezi muli malingaliro kwa anthu okhulupirira |