×

Ndipo aliyense amene amatsutsa ndi kutsutsana ndi Mtumwi, langizo lathu litaonetsedwa kwa 4:115 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:115) ayat 115 in Chichewa

4:115 Surah An-Nisa’ ayat 115 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 115 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿وَمَن يُشَاقِقِ ٱلرَّسُولَ مِنۢ بَعۡدِ مَا تَبَيَّنَ لَهُ ٱلۡهُدَىٰ وَيَتَّبِعۡ غَيۡرَ سَبِيلِ ٱلۡمُؤۡمِنِينَ نُوَلِّهِۦ مَا تَوَلَّىٰ وَنُصۡلِهِۦ جَهَنَّمَۖ وَسَآءَتۡ مَصِيرًا ﴾
[النِّسَاء: 115]

Ndipo aliyense amene amatsutsa ndi kutsutsana ndi Mtumwi, langizo lathu litaonetsedwa kwa iye ndipo atsatira njira imene siili ya anthu okhulupirira, Ife tidzamusunga mnjira imene wasankha ndipo tidzamuotcha iye ku Moto, malo onyansa kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ومن يشاقق الرسول من بعد ما تبين له الهدى ويتبع غير سبيل, باللغة نيانجا

﴿ومن يشاقق الرسول من بعد ما تبين له الهدى ويتبع غير سبيل﴾ [النِّسَاء: 115]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo amene anyoza Mtumiki pambuyo pomuonekera chiongoko, nkutsata njira yosakhala ya okhulupirira, timtembenuzira kumene watembenukira mwini wakeko. Ndipo tidzamulowetsa ku Jahannam. Taonani kuipa malo ofikira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek