×

“Ndithudi ine ndidzawasocheretsa ndipo, ndithudi, ndidzaukitsa zilakolako zawo zopanda pake ndipo, ndithudi, 4:119 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:119) ayat 119 in Chichewa

4:119 Surah An-Nisa’ ayat 119 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 119 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿وَلَأُضِلَّنَّهُمۡ وَلَأُمَنِّيَنَّهُمۡ وَلَأٓمُرَنَّهُمۡ فَلَيُبَتِّكُنَّ ءَاذَانَ ٱلۡأَنۡعَٰمِ وَلَأٓمُرَنَّهُمۡ فَلَيُغَيِّرُنَّ خَلۡقَ ٱللَّهِۚ وَمَن يَتَّخِذِ ٱلشَّيۡطَٰنَ وَلِيّٗا مِّن دُونِ ٱللَّهِ فَقَدۡ خَسِرَ خُسۡرَانٗا مُّبِينٗا ﴾
[النِّسَاء: 119]

“Ndithudi ine ndidzawasocheretsa ndipo, ndithudi, ndidzaukitsa zilakolako zawo zopanda pake ndipo, ndithudi, ndidzawalamula kuboola makutu a ng’ombe ndipo, ndithudi, ndidzawalamula kusintha zinthu zimene zinalengedwa ndi Mulungu.” Ndithudi aliyense amene asankha Satana m’malo mwa Mulungu ngati mtetezi wake, iye ndi wotayika kodziwikiratu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولأضلنهم ولأمنينهم ولآمرنهم فليبتكن آذان الأنعام ولآمرنهم فليغيرن خلق الله ومن يتخذ, باللغة نيانجا

﴿ولأضلنهم ولأمنينهم ولآمرنهم فليبتكن آذان الأنعام ولآمرنهم فليغيرن خلق الله ومن يتخذ﴾ [النِّسَاء: 119]

Khaled Ibrahim Betala
““Ndipo ndikawasokeretsa ndi kuwapatsa ziyembekezo (zabodza) ndithu ndikawalamula kuti azikadula makutu a ziweto, ndipo ndikawalamulanso kuti azikasintha chilengedwe cha Allah.” Ndipo amene angamulole satana kukhala mtetezi wake kusiya Allah, ndiye kuti wataika koonekera
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek