Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 120 - النِّسَاء - Page - Juz 5
﴿يَعِدُهُمۡ وَيُمَنِّيهِمۡۖ وَمَا يَعِدُهُمُ ٱلشَّيۡطَٰنُ إِلَّا غُرُورًا ﴾
[النِّسَاء: 120]
﴿يعدهم ويمنيهم وما يعدهم الشيطان إلا غرورا﴾ [النِّسَاء: 120]
Khaled Ibrahim Betala “(Satana) akuwalonjeza ndikuwapatsa chiyembekezo (pa zinthu zomwe sizingachitike). Ndithudi, satana sawalonjeza china koma chinyengo basi |