×

Chifukwa chakuphwanya pangano lawo ndi kukana zizindikiro za Mulungu ndi kupha Atumwi 4:155 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:155) ayat 155 in Chichewa

4:155 Surah An-Nisa’ ayat 155 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 155 - النِّسَاء - Page - Juz 6

﴿فَبِمَا نَقۡضِهِم مِّيثَٰقَهُمۡ وَكُفۡرِهِم بِـَٔايَٰتِ ٱللَّهِ وَقَتۡلِهِمُ ٱلۡأَنۢبِيَآءَ بِغَيۡرِ حَقّٖ وَقَوۡلِهِمۡ قُلُوبُنَا غُلۡفُۢۚ بَلۡ طَبَعَ ٱللَّهُ عَلَيۡهَا بِكُفۡرِهِمۡ فَلَا يُؤۡمِنُونَ إِلَّا قَلِيلٗا ﴾
[النِّسَاء: 155]

Chifukwa chakuphwanya pangano lawo ndi kukana zizindikiro za Mulungu ndi kupha Atumwi popanda chilungamo ndi kulankhula kwawo koti: Mitima yathu ndi yokutidwa. Iyayi, Mulungu wamata mitima yawo chifukwa chakusakhulupirira kwawo. Ndipo iwo sakhulupirira kwenikweni koma pang’ono

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فبما نقضهم ميثاقهم وكفرهم بآيات الله وقتلهم الأنبياء بغير حق وقولهم قلوبنا, باللغة نيانجا

﴿فبما نقضهم ميثاقهم وكفرهم بآيات الله وقتلهم الأنبياء بغير حق وقولهم قلوبنا﴾ [النِّسَاء: 155]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho (tidawalanga) chifukwa chakuswa mapangano awo, ndi kukana kwawo zisonyezo za Allah, ndi kupha kwawo aneneri popanda choonadi, ndi kunena kwawo kwakuti: “Mitima yathu yakutidwa (siingathe kuzindikira zomwe ukunena iwe Muhammad {s.a.w}).” (Ai, Siinakutidwe ndi chilichonse), koma Allah waidinda zidindo chifukwa cha kusakhulupirira kwawo; tero sakhulupirira koma pang’ono pokha
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek