×

Pokwaniritsa lonjezo, Ife tidakweza pamwamba pawo phiri, ndipo tidati kwa iwo: “Lowani 4:154 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:154) ayat 154 in Chichewa

4:154 Surah An-Nisa’ ayat 154 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 154 - النِّسَاء - Page - Juz 6

﴿وَرَفَعۡنَا فَوۡقَهُمُ ٱلطُّورَ بِمِيثَٰقِهِمۡ وَقُلۡنَا لَهُمُ ٱدۡخُلُواْ ٱلۡبَابَ سُجَّدٗا وَقُلۡنَا لَهُمۡ لَا تَعۡدُواْ فِي ٱلسَّبۡتِ وَأَخَذۡنَا مِنۡهُم مِّيثَٰقًا غَلِيظٗا ﴾
[النِّسَاء: 154]

Pokwaniritsa lonjezo, Ife tidakweza pamwamba pawo phiri, ndipo tidati kwa iwo: “Lowani pa chipata mogwetsa nkhope ndi modzichepetsa.” Ndipo Ife tidawalamula kuti: “Musaswe malamulo a tsiku la Sabata.” Ndipo Ife tidatenga lonjezo lokhazikika kuchokera kwa iwo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ورفعنا فوقهم الطور بميثاقهم وقلنا لهم ادخلوا الباب سجدا وقلنا لهم لا, باللغة نيانجا

﴿ورفعنا فوقهم الطور بميثاقهم وقلنا لهم ادخلوا الباب سجدا وقلنا لهم لا﴾ [النِّسَاء: 154]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo tidatukula phiri la Al-Tur pamwamba pawo (Ayudawo) polandira pangano lawo; tidati kwa iwo: “Lowani pachipata (cha dziko ili la Sham) mutawerama.” Tidatinso kwa iwo: “Musalumphe malire pa nkhani ya Sabata.” Ndipo tidalandira kwa iwo pangano lokhwima
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek