×

oh inu anthu okhulupirira! Musadye chuma cha anzanu mopanda chilungamo ngakhale kuti 4:29 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:29) ayat 29 in Chichewa

4:29 Surah An-Nisa’ ayat 29 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 29 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ لَا تَأۡكُلُوٓاْ أَمۡوَٰلَكُم بَيۡنَكُم بِٱلۡبَٰطِلِ إِلَّآ أَن تَكُونَ تِجَٰرَةً عَن تَرَاضٖ مِّنكُمۡۚ وَلَا تَقۡتُلُوٓاْ أَنفُسَكُمۡۚ إِنَّ ٱللَّهَ كَانَ بِكُمۡ رَحِيمٗا ﴾
[النِّسَاء: 29]

oh inu anthu okhulupirira! Musadye chuma cha anzanu mopanda chilungamo ngakhale kuti ndi malonda amene mwagwirizana pakati panu. Ndipo musawonongane wina ndi mzake. Ndithudi Mulungu ndi wa chifundo chosatha kwa inu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها الذين آمنوا لا تأكلوا أموالكم بينكم بالباطل إلا أن تكون تجارة, باللغة نيانجا

﴿ياأيها الذين آمنوا لا تأكلوا أموالكم بينكم بالباطل إلا أن تكون تجارة﴾ [النِّسَاء: 29]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu amene mwakhulupirira! Musadye chuma chanu mwachinyengo koma m’njira yamalonda ndi moyanjana pakati panu. Ndipo musadziphe nokha (ngakhale kupha anzanu). Ndithudi, Allah ali Wachisoni pa inu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek