Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 28 - النِّسَاء - Page - Juz 5
﴿يُرِيدُ ٱللَّهُ أَن يُخَفِّفَ عَنكُمۡۚ وَخُلِقَ ٱلۡإِنسَٰنُ ضَعِيفٗا ﴾
[النِّسَاء: 28]
﴿يريد الله أن يخفف عنكم وخلق الإنسان ضعيفا﴾ [النِّسَاء: 28]
Khaled Ibrahim Betala “Allah akufuna kukupeputsirani, pakuti munthu adalengedwa wofooka (alibe mphamvu za thupi ngakhale zolimbana ndi zilakolako za moyo) |