×

Ngati inu mupewa machimo akuluakulu amene mukuletsedwa, Ife tidzakukhululukirani machimo anu ndipo 4:31 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:31) ayat 31 in Chichewa

4:31 Surah An-Nisa’ ayat 31 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 31 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿إِن تَجۡتَنِبُواْ كَبَآئِرَ مَا تُنۡهَوۡنَ عَنۡهُ نُكَفِّرۡ عَنكُمۡ سَيِّـَٔاتِكُمۡ وَنُدۡخِلۡكُم مُّدۡخَلٗا كَرِيمٗا ﴾
[النِّسَاء: 31]

Ngati inu mupewa machimo akuluakulu amene mukuletsedwa, Ife tidzakukhululukirani machimo anu ndipo tidzakulowetsani kukhomo lolemekezeka

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن تجتنبوا كبائر ما تنهون عنه نكفر عنكم سيئاتكم وندخلكم مدخلا كريما, باللغة نيانجا

﴿إن تجتنبوا كبائر ما تنهون عنه نكفر عنكم سيئاتكم وندخلكم مدخلا كريما﴾ [النِّسَاء: 31]

Khaled Ibrahim Betala
“Ngati mudzitalikitsa kumachimo akuluakulu omwe mukuletsedwa, ndiye kuti tikufafanizirani zolakwa zanu (zing’onozing’ono) ndipo tidzakulowetsani malo aulemu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek