Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 55 - النِّسَاء - Page - Juz 5
﴿فَمِنۡهُم مَّنۡ ءَامَنَ بِهِۦ وَمِنۡهُم مَّن صَدَّ عَنۡهُۚ وَكَفَىٰ بِجَهَنَّمَ سَعِيرًا ﴾
[النِّسَاء: 55]
﴿فمنهم من آمن به ومنهم من صد عنه وكفى بجهنم سعيرا﴾ [النِّسَاء: 55]
Khaled Ibrahim Betala “Choncho alipo ena mwa iwo amene anazikhulupirira izi, ndiponso alipo ena mwa iwo omwe adziika nazo kutali. Ndipo Jahannam ikukwanira kukhala Moto waukali wowatentha |