×

Ndithudi iwo amene adakana zizindikiro zathu tidzawaotcha ku moto. Nthawi zonse pamene 4:56 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:56) ayat 56 in Chichewa

4:56 Surah An-Nisa’ ayat 56 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 56 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ بِـَٔايَٰتِنَا سَوۡفَ نُصۡلِيهِمۡ نَارٗا كُلَّمَا نَضِجَتۡ جُلُودُهُم بَدَّلۡنَٰهُمۡ جُلُودًا غَيۡرَهَا لِيَذُوقُواْ ٱلۡعَذَابَۗ إِنَّ ٱللَّهَ كَانَ عَزِيزًا حَكِيمٗا ﴾
[النِّسَاء: 56]

Ndithudi iwo amene adakana zizindikiro zathu tidzawaotcha ku moto. Nthawi zonse pamene makungu awo azidzapsya, Ife tidzawapatsa makungu ena kuti iwo alawe chilango. Ndithudi Mulungu ndi wamphamvu nthawi zonse ndi Wanzeru

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الذين كفروا بآياتنا سوف نصليهم نارا كلما نضجت جلودهم بدلناهم جلودا, باللغة نيانجا

﴿إن الذين كفروا بآياتنا سوف نصليهم نارا كلما نضجت جلودهم بدلناهم جلودا﴾ [النِّسَاء: 56]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu amene sadakhulupirire zizindikiro Zathu, tidzawalowetsa ku Moto. Nthawi iliyonse yomwe makungu awo adzikapselera tidzidzawasinthira makungu ena kuti adzapitirize kulawa chilango. Ndithudi, Allah Ngwamphamvu zoposa, Ngwanzeru zakuya
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek