Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 71 - النِّسَاء - Page - Juz 5
﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ خُذُواْ حِذۡرَكُمۡ فَٱنفِرُواْ ثُبَاتٍ أَوِ ٱنفِرُواْ جَمِيعٗا ﴾
[النِّسَاء: 71]
﴿ياأيها الذين آمنوا خذوا حذركم فانفروا ثبات أو انفروا جميعا﴾ [النِّسَاء: 71]
Khaled Ibrahim Betala “E inu amene mwakhulupirira! Khalani ochenjera (ndi adani anu; musanyengedwe nawo). Pitani (kunkhondo) gulu limodzilimodzi, kapena pitaniko nonsenu pamodzi (monga momwe Mtumiki angakulangizireni) |