Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 72 - النِّسَاء - Page - Juz 5
﴿وَإِنَّ مِنكُمۡ لَمَن لَّيُبَطِّئَنَّ فَإِنۡ أَصَٰبَتۡكُم مُّصِيبَةٞ قَالَ قَدۡ أَنۡعَمَ ٱللَّهُ عَلَيَّ إِذۡ لَمۡ أَكُن مَّعَهُمۡ شَهِيدٗا ﴾
[النِّسَاء: 72]
﴿وإن منكم لمن ليبطئن فإن أصابتكم مصيبة قال قد أنعم الله علي﴾ [النِّسَاء: 72]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ndithu alipo ena mwa inu otsalira m’mbuyo sapita ku nkhondo, (ndiponso amaletsa anzawo). Ngati vuto litakupezani, (yense wa iwo) amanena: “Allah wandichitira chisomo posakhala m’gulu lawo kumeneko.” |