×

Ndi chinthu choletsedwa kuti munthu wokhulupirira aphe mzake wokhulupirira kupatula mwangozi. Ndipo 4:92 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:92) ayat 92 in Chichewa

4:92 Surah An-Nisa’ ayat 92 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 92 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿وَمَا كَانَ لِمُؤۡمِنٍ أَن يَقۡتُلَ مُؤۡمِنًا إِلَّا خَطَـٔٗاۚ وَمَن قَتَلَ مُؤۡمِنًا خَطَـٔٗا فَتَحۡرِيرُ رَقَبَةٖ مُّؤۡمِنَةٖ وَدِيَةٞ مُّسَلَّمَةٌ إِلَىٰٓ أَهۡلِهِۦٓ إِلَّآ أَن يَصَّدَّقُواْۚ فَإِن كَانَ مِن قَوۡمٍ عَدُوّٖ لَّكُمۡ وَهُوَ مُؤۡمِنٞ فَتَحۡرِيرُ رَقَبَةٖ مُّؤۡمِنَةٖۖ وَإِن كَانَ مِن قَوۡمِۭ بَيۡنَكُمۡ وَبَيۡنَهُم مِّيثَٰقٞ فَدِيَةٞ مُّسَلَّمَةٌ إِلَىٰٓ أَهۡلِهِۦ وَتَحۡرِيرُ رَقَبَةٖ مُّؤۡمِنَةٖۖ فَمَن لَّمۡ يَجِدۡ فَصِيَامُ شَهۡرَيۡنِ مُتَتَابِعَيۡنِ تَوۡبَةٗ مِّنَ ٱللَّهِۗ وَكَانَ ٱللَّهُ عَلِيمًا حَكِيمٗا ﴾
[النِّسَاء: 92]

Ndi chinthu choletsedwa kuti munthu wokhulupirira aphe mzake wokhulupirira kupatula mwangozi. Ndipo aliyense amene, mwangozi, akupha munthu wokhulupirira ayenera kumasula kapolo wokhulupirira m’modzi ndi kulipira ndalama zopepesera ku banja la ophedwayo, kupatula ngati iwo asankha kuti amukhululukira munthu wakuphayo. Ngati malemuyo anali wochokera kwa adani anu ndipo anali wokhulupirira, chilango chake ndi kumasula kapolo m’modzi wa wokhulupirira. Koma ngati malemuyo anali ochokera ku mtundu wa athu ogwirizana nawo, ndalama za chipepeso ziyenera kuperekedwa kubanja la munthu wakufayo ndi kumasula kapolo mmodzi wa wokhulupirira. Ngati munthu sangathe kupeza izi, ayenera kusala miyezi iwiri motsatizana ndi cholinga chopeza chikhululukiro kwa Mulungu. Ndipo Mulungu ndi Wodziwa ndi Waluntha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما كان لمؤمن أن يقتل مؤمنا إلا خطأ ومن قتل مؤمنا خطأ, باللغة نيانجا

﴿وما كان لمؤمن أن يقتل مؤمنا إلا خطأ ومن قتل مؤمنا خطأ﴾ [النِّسَاء: 92]

❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek