×

Ndipo aliyense amene apha munthu wokhulupirira mwadala, mphotho yake ndi kupsya ku 4:93 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:93) ayat 93 in Chichewa

4:93 Surah An-Nisa’ ayat 93 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 93 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿وَمَن يَقۡتُلۡ مُؤۡمِنٗا مُّتَعَمِّدٗا فَجَزَآؤُهُۥ جَهَنَّمُ خَٰلِدٗا فِيهَا وَغَضِبَ ٱللَّهُ عَلَيۡهِ وَلَعَنَهُۥ وَأَعَدَّ لَهُۥ عَذَابًا عَظِيمٗا ﴾
[النِّسَاء: 93]

Ndipo aliyense amene apha munthu wokhulupirira mwadala, mphotho yake ndi kupsya ku moto wa ku Gahena ndipo adzakhala komweko ndipo mkwiyo ndi temberero la Mulungu zili pa iye ndipo chilango chowawa chili kukonzedwa chifukwa cha iye

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ومن يقتل مؤمنا متعمدا فجزاؤه جهنم خالدا فيها وغضب الله عليه ولعنه, باللغة نيانجا

﴿ومن يقتل مؤمنا متعمدا فجزاؤه جهنم خالدا فيها وغضب الله عليه ولعنه﴾ [النِّسَاء: 93]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo amene angaphe wokhulupilila mwadala, mphoto yake ndi Jahannam; mmenemo adzakhala nthawi yaitali. Ndipo Allah amkwiira ndi kumtembelera ndi kumkonzera chilango chachikulu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek