Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 96 - النِّسَاء - Page - Juz 5
﴿دَرَجَٰتٖ مِّنۡهُ وَمَغۡفِرَةٗ وَرَحۡمَةٗۚ وَكَانَ ٱللَّهُ غَفُورٗا رَّحِيمًا ﴾ 
[النِّسَاء: 96]
﴿درجات منه ومغفرة ورحمة وكان الله غفورا رحيما﴾ [النِّسَاء: 96]
| Khaled Ibrahim Betala “Adzapata nyota zazikulu zochokera kwa Iye ndi chikhululuko ndi chisoni. Ndipo Allah Ngokhululuka kwambiri, Ngwachisoni zedi |