Quran with Chichewa translation - Surah Ghafir ayat 20 - غَافِر - Page - Juz 24
﴿وَٱللَّهُ يَقۡضِي بِٱلۡحَقِّۖ وَٱلَّذِينَ يَدۡعُونَ مِن دُونِهِۦ لَا يَقۡضُونَ بِشَيۡءٍۗ إِنَّ ٱللَّهَ هُوَ ٱلسَّمِيعُ ٱلۡبَصِيرُ ﴾ 
[غَافِر: 20]
﴿والله يقضي بالحق والذين يدعون من دونه لا يقضون بشيء إن الله﴾ [غَافِر: 20]
| Khaled Ibrahim Betala “Ndipo Allah amaweruza mwa chilungamo. Koma omwe akuwapembedza kusiya Allah, saweruza chilichonse (chifukwa cha kufooka ndi kulephera kwawo). Ndithu Allah Yekha ndiye Wakumva, Woona (chilichonse) |