Quran with Chichewa translation - Surah Ghafir ayat 4 - غَافِر - Page - Juz 24
﴿مَا يُجَٰدِلُ فِيٓ ءَايَٰتِ ٱللَّهِ إِلَّا ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ فَلَا يَغۡرُرۡكَ تَقَلُّبُهُمۡ فِي ٱلۡبِلَٰدِ ﴾
[غَافِر: 4]
﴿ما يجادل في آيات الله إلا الذين كفروا فلا يغررك تقلبهم في﴾ [غَافِر: 4]
Khaled Ibrahim Betala “Sangatsutsane pa zisonyezo za Allah kupatula amene akanira. Choncho kusakunyenge kuyendayenda kwawo pa dziko (kunka nachita malonda ndi kupeza phindu lalikulu ndi malondawo popanda chovuta; posachedwa tiwalanga) |