Quran with Chichewa translation - Surah Ghafir ayat 45 - غَافِر - Page - Juz 24
﴿فَوَقَىٰهُ ٱللَّهُ سَيِّـَٔاتِ مَا مَكَرُواْۖ وَحَاقَ بِـَٔالِ فِرۡعَوۡنَ سُوٓءُ ٱلۡعَذَابِ ﴾
[غَافِر: 45]
﴿فوقاه الله سيئات ما مكروا وحاق بآل فرعون سوء العذاب﴾ [غَافِر: 45]
Khaled Ibrahim Betala “Choncho Allah adam’teteza ku zoipa zomwe adam’tchera. Ndipo chilango choipa chidawazungulira anthu a Farawo (pamodzi ndi iye mwini) |