×

Kotero pirira. Ndithudi lonjezo la Mulungu ndi loona. Ndipo pempha chikhululukiro cha 40:55 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ghafir ⮕ (40:55) ayat 55 in Chichewa

40:55 Surah Ghafir ayat 55 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ghafir ayat 55 - غَافِر - Page - Juz 24

﴿فَٱصۡبِرۡ إِنَّ وَعۡدَ ٱللَّهِ حَقّٞ وَٱسۡتَغۡفِرۡ لِذَنۢبِكَ وَسَبِّحۡ بِحَمۡدِ رَبِّكَ بِٱلۡعَشِيِّ وَٱلۡإِبۡكَٰرِ ﴾
[غَافِر: 55]

Kotero pirira. Ndithudi lonjezo la Mulungu ndi loona. Ndipo pempha chikhululukiro cha machimo ako ndipo lemekeza Ambuye wako madzulo ndi m’mawa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فاصبر إن وعد الله حق واستغفر لذنبك وسبح بحمد ربك بالعشي والإبكار, باللغة نيانجا

﴿فاصبر إن وعد الله حق واستغفر لذنبك وسبح بحمد ربك بالعشي والإبكار﴾ [غَافِر: 55]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho pirira, ndithu lonjezo la Allah ndi loona. Ndipo pempha chikhululuko cha machimo ako (ukachimwa), ndipo lemekeza Mbuye wako ndi kumtamanda madzulo ndi m’mawa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek