Quran with Chichewa translation - Surah Ghafir ayat 6 - غَافِر - Page - Juz 24
﴿وَكَذَٰلِكَ حَقَّتۡ كَلِمَتُ رَبِّكَ عَلَى ٱلَّذِينَ كَفَرُوٓاْ أَنَّهُمۡ أَصۡحَٰبُ ٱلنَّارِ ﴾
[غَافِر: 6]
﴿وكذلك حقت كلمة ربك على الذين كفروا أنهم أصحاب النار﴾ [غَافِر: 6]
Khaled Ibrahim Betala “Chonchonso latsimikizika liwu la chilango pa amene akanira (iwe Mtumiki {s.a.w}) chifukwa iwo ndi anthu a ku Moto (kamba kosankhakukanira ndi kusiya kukhulupirira) |