×

Ndipo Ambuye wako adati, “Ndipempheni Ine ndipo ndidzayankha pemphero lanu. Ndithudi! Koma 40:60 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ghafir ⮕ (40:60) ayat 60 in Chichewa

40:60 Surah Ghafir ayat 60 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ghafir ayat 60 - غَافِر - Page - Juz 24

﴿وَقَالَ رَبُّكُمُ ٱدۡعُونِيٓ أَسۡتَجِبۡ لَكُمۡۚ إِنَّ ٱلَّذِينَ يَسۡتَكۡبِرُونَ عَنۡ عِبَادَتِي سَيَدۡخُلُونَ جَهَنَّمَ دَاخِرِينَ ﴾
[غَافِر: 60]

Ndipo Ambuye wako adati, “Ndipempheni Ine ndipo ndidzayankha pemphero lanu. Ndithudi! Koma iwo amene ndi amwano pondipembedza Ine, ndithudi, adzaponyedwa ku Gahena mochititsa manyazi.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقال ربكم ادعوني أستجب لكم إن الذين يستكبرون عن عبادتي سيدخلون جهنم, باللغة نيانجا

﴿وقال ربكم ادعوني أستجب لكم إن الذين يستكبرون عن عبادتي سيدخلون جهنم﴾ [غَافِر: 60]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo Mbuye wanu wanena: “Ndipempheni, ndikuyankhani; koma amene akudzikweza posiya kundipembedza, adzalowa ku Jahannam ali oyaluka.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek