×

Ndipo iwo adzati kwa makungu awo, “Bwanji inu muli kupereka umboni wotineneza?” 41:21 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Fussilat ⮕ (41:21) ayat 21 in Chichewa

41:21 Surah Fussilat ayat 21 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 21 - فُصِّلَت - Page - Juz 24

﴿وَقَالُواْ لِجُلُودِهِمۡ لِمَ شَهِدتُّمۡ عَلَيۡنَاۖ قَالُوٓاْ أَنطَقَنَا ٱللَّهُ ٱلَّذِيٓ أَنطَقَ كُلَّ شَيۡءٖۚ وَهُوَ خَلَقَكُمۡ أَوَّلَ مَرَّةٖ وَإِلَيۡهِ تُرۡجَعُونَ ﴾
[فُصِّلَت: 21]

Ndipo iwo adzati kwa makungu awo, “Bwanji inu muli kupereka umboni wotineneza?” Iwo adzati, “Mulungu, amene amayankhulitsa chilichonse, watiyankhulitsa ife ndipo Iye ndiye amene adakulengani inu poyamba ndipo nonse mudzabwerera kwa Iye.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقالوا لجلودهم لم شهدتم علينا قالوا أنطقنا الله الذي أنطق كل شيء, باللغة نيانجا

﴿وقالوا لجلودهم لم شهدتم علينا قالوا أنطقنا الله الذي أنطق كل شيء﴾ [فُصِّلَت: 21]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo adzanena (adani a Allah) ku makungu awo: “Bwanji mukutiperekera umboni woipa?” Zidzati: “Allah watiyankhulitsa, Amene amayankhulitsa chilichonse; ndipo Iye ndi Amene adakulengani (mkulenga) koyamba (pomwe simudali kanthu), ndiponso kwa Iye Yekha ndiko mudzabwezedwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek