×

Ndipo Ife tawasankhira anzawo amene adapanga kuti aziona zopusa zakale ndi zatsopano 41:25 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Fussilat ⮕ (41:25) ayat 25 in Chichewa

41:25 Surah Fussilat ayat 25 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 25 - فُصِّلَت - Page - Juz 24

﴿۞ وَقَيَّضۡنَا لَهُمۡ قُرَنَآءَ فَزَيَّنُواْ لَهُم مَّا بَيۡنَ أَيۡدِيهِمۡ وَمَا خَلۡفَهُمۡ وَحَقَّ عَلَيۡهِمُ ٱلۡقَوۡلُ فِيٓ أُمَمٖ قَدۡ خَلَتۡ مِن قَبۡلِهِم مِّنَ ٱلۡجِنِّ وَٱلۡإِنسِۖ إِنَّهُمۡ كَانُواْ خَٰسِرِينَ ﴾
[فُصِّلَت: 25]

Ndipo Ife tawasankhira anzawo amene adapanga kuti aziona zopusa zakale ndi zatsopano kukhala zinthu zokondweretsa kwa iwo. Ndipo chiweruzo chimene chidadza ku mtundu wa majini ndi kwa anthu amene adalipo kale chakwaniritsidwa kwa iwo. Ndithudi iwo ndi otayika kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقيضنا لهم قرناء فزينوا لهم ما بين أيديهم وما خلفهم وحق عليهم, باللغة نيانجا

﴿وقيضنا لهم قرناء فزينوا لهم ما بين أيديهم وما خلفهم وحق عليهم﴾ [فُصِّلَت: 25]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo tidawakonzera iwo abwenzi oipa (padziko lapansi), choncho adawakometsera zamtsogolo mwawo ndi za pambuyo pawo ndipo liwu la chilango lidatsimikizika pa iwo pamodzi ndi mibadwo yomwe idapita kale ya ziwanda ndi anthu, ndithu iwo adali otaika
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek