×

Ndipo ngati iwo apirira komabe ku moto ndiko kudzakhala kumalo kwawo. Ndipo 41:24 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Fussilat ⮕ (41:24) ayat 24 in Chichewa

41:24 Surah Fussilat ayat 24 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 24 - فُصِّلَت - Page - Juz 24

﴿فَإِن يَصۡبِرُواْ فَٱلنَّارُ مَثۡوٗى لَّهُمۡۖ وَإِن يَسۡتَعۡتِبُواْ فَمَا هُم مِّنَ ٱلۡمُعۡتَبِينَ ﴾
[فُصِّلَت: 24]

Ndipo ngati iwo apirira komabe ku moto ndiko kudzakhala kumalo kwawo. Ndipo ngati apempha chikhululukiro pempho lawo lidzakanidwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فإن يصبروا فالنار مثوى لهم وإن يستعتبوا فما هم من المعتبين, باللغة نيانجا

﴿فإن يصبروا فالنار مثوى لهم وإن يستعتبوا فما هم من المعتبين﴾ [فُصِّلَت: 24]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho ngakhalc atapirira (ku zopweteka zawo), moto ndiwo mabwelero awo ndi kokhazikika kwawo kwa muyaya. Ngati atapempha chiyanjo cha Allah pa iwo, iwo sadzakhala m’gulu la oyanjidwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek