×

Koma, ndithudi, Ife tidzawalawitsa anthu osakhulupirira chilango chowawa, ndipo, ndithudi, Ife tidzawalipira 41:27 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Fussilat ⮕ (41:27) ayat 27 in Chichewa

41:27 Surah Fussilat ayat 27 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 27 - فُصِّلَت - Page - Juz 24

﴿فَلَنُذِيقَنَّ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ عَذَابٗا شَدِيدٗا وَلَنَجۡزِيَنَّهُمۡ أَسۡوَأَ ٱلَّذِي كَانُواْ يَعۡمَلُونَ ﴾
[فُصِّلَت: 27]

Koma, ndithudi, Ife tidzawalawitsa anthu osakhulupirira chilango chowawa, ndipo, ndithudi, Ife tidzawalipira chifukwa cha ntchito zawo zoipa zimene anali kuchita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فلنذيقن الذين كفروا عذابا شديدا ولنجزينهم أسوأ الذي كانوا يعملون, باللغة نيانجا

﴿فلنذيقن الذين كفروا عذابا شديدا ولنجزينهم أسوأ الذي كانوا يعملون﴾ [فُصِّلَت: 27]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu tiwalawitsa amene akanira chilango choopsa (pa zochita zawo zoipa, makamaka pakuithira Qur’an nkhondo), ndipo ndithu tiwalipira malipiro oipitsitsa chifukwa cha zoipa zomwe adali kuchita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek