Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 28 - فُصِّلَت - Page - Juz 24
﴿ذَٰلِكَ جَزَآءُ أَعۡدَآءِ ٱللَّهِ ٱلنَّارُۖ لَهُمۡ فِيهَا دَارُ ٱلۡخُلۡدِ جَزَآءَۢ بِمَا كَانُواْ بِـَٔايَٰتِنَا يَجۡحَدُونَ ﴾
[فُصِّلَت: 28]
﴿ذلك جزاء أعداء الله النار لهم فيها دار الخلد جزاء بما كانوا﴾ [فُصِّلَت: 28]
Khaled Ibrahim Betala “Imeneyo ndi mphoto yoyenera ya adani a Allah, yomwe ndi Moto. Mmenemo adzakhala muyaya. Imeneyi ndi mphoto ya zimene adali kuzikanira m’zisonyezo Zathu |