×

Ndipo iwo osakhulupirira adzati, “Ambuye wathu! Tilangizeni iwo amene ali pakati pa 41:29 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Fussilat ⮕ (41:29) ayat 29 in Chichewa

41:29 Surah Fussilat ayat 29 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 29 - فُصِّلَت - Page - Juz 24

﴿وَقَالَ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ رَبَّنَآ أَرِنَا ٱلَّذَيۡنِ أَضَلَّانَا مِنَ ٱلۡجِنِّ وَٱلۡإِنسِ نَجۡعَلۡهُمَا تَحۡتَ أَقۡدَامِنَا لِيَكُونَا مِنَ ٱلۡأَسۡفَلِينَ ﴾
[فُصِّلَت: 29]

Ndipo iwo osakhulupirira adzati, “Ambuye wathu! Tilangizeni iwo amene ali pakati pa majini ndi anthu amene adatisocheretsa ife ndipo ife tidzawapondaponda ndi mapazi athu kuti iwo akhale a pansi kwambiri.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقال الذين كفروا ربنا أرنا اللذين أضلانا من الجن والإنس نجعلهما تحت, باللغة نيانجا

﴿وقال الذين كفروا ربنا أرنا اللذين أضلانا من الجن والإنس نجعلهما تحت﴾ [فُصِّلَت: 29]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo okanira adzanena (ali mkati mwa Moto): “E Mbuye wathu! Tisonyezeni (magulu awiri) amene adatisokeretsa ochokera m’ziwanda ndi anthu kuti tiwaike pansi pa mapazi athu, kuti akhale mwa apansi (mu ulemelero ndi malo).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek