Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 30 - فُصِّلَت - Page - Juz 24
﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ قَالُواْ رَبُّنَا ٱللَّهُ ثُمَّ ٱسۡتَقَٰمُواْ تَتَنَزَّلُ عَلَيۡهِمُ ٱلۡمَلَٰٓئِكَةُ أَلَّا تَخَافُواْ وَلَا تَحۡزَنُواْ وَأَبۡشِرُواْ بِٱلۡجَنَّةِ ٱلَّتِي كُنتُمۡ تُوعَدُونَ ﴾
[فُصِّلَت: 30]
﴿إن الذين قالوا ربنا الله ثم استقاموا تتنـزل عليهم الملائكة ألا تخافوا﴾ [فُصِّلَت: 30]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu amene anena (kuti): “Mbuye wathu ndi Allah,” (povomereza umodzi Wake), kenako nkupitiriza kulungama pa malamulo Ake, angelo amawatsikira iwo nthawi yakufa (uku akuti): “Musaope (pa zomwe mukumane nazo). Ndipo musadandaule (pazomwe mwazisiya). Ndipo sangalalani ndi Munda wamtendere umene mudalonjezedwa (kupyolera mmalirime a aneneri).” |