Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 31 - فُصِّلَت - Page - Juz 24
﴿نَحۡنُ أَوۡلِيَآؤُكُمۡ فِي ٱلۡحَيَوٰةِ ٱلدُّنۡيَا وَفِي ٱلۡأٓخِرَةِۖ وَلَكُمۡ فِيهَا مَا تَشۡتَهِيٓ أَنفُسُكُمۡ وَلَكُمۡ فِيهَا مَا تَدَّعُونَ ﴾
[فُصِّلَت: 31]
﴿نحن أولياؤكم في الحياة الدنيا وفي الآخرة ولكم فيها ما تشتهي أنفسكم﴾ [فُصِّلَت: 31]
Khaled Ibrahim Betala “(Angelo amanena kwa iwo): “Ife ndi athangati anu pamoyo wa pa dziko lapansi (pokulimbikitsani panjira yolungama), ndi tsiku lachimaliziro (pokupempherani chipulumutso kwa Allah); inu mukapeza kumeneko chilichonse chomwe mitima yanu ikafune (zokoma ndi zabwino); ndipo, mukapeza mmenemo chilichonse chomwe mukachilakelake.” |