Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 33 - فُصِّلَت - Page - Juz 24
﴿وَمَنۡ أَحۡسَنُ قَوۡلٗا مِّمَّن دَعَآ إِلَى ٱللَّهِ وَعَمِلَ صَٰلِحٗا وَقَالَ إِنَّنِي مِنَ ٱلۡمُسۡلِمِينَ ﴾
[فُصِّلَت: 33]
﴿ومن أحسن قولا ممن دعا إلى الله وعمل صالحا وقال إنني من﴾ [فُصِّلَت: 33]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi ndani yemwe ali ndi zonena zabwino kuposa yemwe akuitanira kwa Allah (ndi kumumvera), ndikuchita, (pamodzi ndi zimenezo), zabwino uku akunena: “Ine ndi mmodzi mwa ogonjera (malamulo a Allah).” |