Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 34 - فُصِّلَت - Page - Juz 24
﴿وَلَا تَسۡتَوِي ٱلۡحَسَنَةُ وَلَا ٱلسَّيِّئَةُۚ ٱدۡفَعۡ بِٱلَّتِي هِيَ أَحۡسَنُ فَإِذَا ٱلَّذِي بَيۡنَكَ وَبَيۡنَهُۥ عَدَٰوَةٞ كَأَنَّهُۥ وَلِيٌّ حَمِيمٞ ﴾
[فُصِّلَت: 34]
﴿ولا تستوي الحسنة ولا السيئة ادفع بالتي هي أحسن فإذا الذي بينك﴾ [فُصِّلَت: 34]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo chabwino sichingafanane ndi choipa. Chotsa (choipa) ndi chomwe chili chabwino; mapeto ake akhala kuti yemwe padali chidani pakati pako ndi pakati pake (akhala) ngati mthandizi wodalirika |