×

Ndithudi iwo amene amakana uthenga pamene udza kwa iwo adzalangidwa. Ndithudi ili 41:41 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Fussilat ⮕ (41:41) ayat 41 in Chichewa

41:41 Surah Fussilat ayat 41 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 41 - فُصِّلَت - Page - Juz 24

﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ بِٱلذِّكۡرِ لَمَّا جَآءَهُمۡۖ وَإِنَّهُۥ لَكِتَٰبٌ عَزِيزٞ ﴾
[فُصِّلَت: 41]

Ndithudi iwo amene amakana uthenga pamene udza kwa iwo adzalangidwa. Ndithudi ili ndi Buku lolemekezeka kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الذين كفروا بالذكر لما جاءهم وإنه لكتاب عزيز, باللغة نيانجا

﴿إن الذين كفروا بالذكر لما جاءهم وإنه لكتاب عزيز﴾ [فُصِّلَت: 41]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu amene atsutsa Qur’an yolemekezeka ikawadzera (popanda kulingalira, kwa iwo kudzakhala chilango chosasimbika). Ndipo ndithu limeneli ndi buku lopambana (chilichonse cholipinga)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek