Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 42 - فُصِّلَت - Page - Juz 24
﴿لَّا يَأۡتِيهِ ٱلۡبَٰطِلُ مِنۢ بَيۡنِ يَدَيۡهِ وَلَا مِنۡ خَلۡفِهِۦۖ تَنزِيلٞ مِّنۡ حَكِيمٍ حَمِيدٖ ﴾
[فُصِّلَت: 42]
﴿لا يأتيه الباطل من بين يديه ولا من خلفه تنـزيل من حكيم﴾ [فُصِّلَت: 42]
Khaled Ibrahim Betala “Silifikidwa ndi chonama patsogolo pake ngakhale pambuyo pake. Ndi lovumbulutsidwa kuchokera kwa Wanzeru zakuya, Woyamikidwa kwambiri (mzochita Zake) |