Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 47 - فُصِّلَت - Page - Juz 25
﴿۞ إِلَيۡهِ يُرَدُّ عِلۡمُ ٱلسَّاعَةِۚ وَمَا تَخۡرُجُ مِن ثَمَرَٰتٖ مِّنۡ أَكۡمَامِهَا وَمَا تَحۡمِلُ مِنۡ أُنثَىٰ وَلَا تَضَعُ إِلَّا بِعِلۡمِهِۦۚ وَيَوۡمَ يُنَادِيهِمۡ أَيۡنَ شُرَكَآءِي قَالُوٓاْ ءَاذَنَّٰكَ مَا مِنَّا مِن شَهِيدٖ ﴾
[فُصِّلَت: 47]
﴿إليه يرد علم الساعة وما تخرج من ثمرات من أكمامها وما تحمل﴾ [فُصِّلَت: 47]
Khaled Ibrahim Betala “۞ Kudziwa kwa tsiku la Qiyâma kukubwezedwa kwa Iye (Allah;) zipatso sizituluka m’mikoko yake ndipo mkazi satenga pakati ndi kubereka popanda Allah kudziwa. (Koma amadziwa zonsezo bwinobwino). Ndipo (kumbukira) tsiku limene Allah adzawaitane (ndi kuwafunsa kuti): “Ali kuti aphatikizi Anga aja (amene mudali kuwapembedza kusiya Ine)?” Adzanena (modandaula): “Tikukudziwitsani, (E Inu Allah)! Palibe aliyense mwa ife angaikire umboni (kuti Inu muli ndi mnzanu).” |