×

Aliyense amene amachita zabwino amachitira moyo wake zabwino ndipo aliyense amene amachita 41:46 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Fussilat ⮕ (41:46) ayat 46 in Chichewa

41:46 Surah Fussilat ayat 46 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 46 - فُصِّلَت - Page - Juz 24

﴿مَّنۡ عَمِلَ صَٰلِحٗا فَلِنَفۡسِهِۦۖ وَمَنۡ أَسَآءَ فَعَلَيۡهَاۗ وَمَا رَبُّكَ بِظَلَّٰمٖ لِّلۡعَبِيدِ ﴾
[فُصِّلَت: 46]

Aliyense amene amachita zabwino amachitira moyo wake zabwino ndipo aliyense amene amachita zoipa amadzikundikira yekha mavuto. Ndithudi Ambuye wako sapondereza akapolo ake

❮ Previous Next ❯

ترجمة: من عمل صالحا فلنفسه ومن أساء فعليها وما ربك بظلام للعبيد, باللغة نيانجا

﴿من عمل صالحا فلنفسه ومن أساء فعليها وما ربك بظلام للعبيد﴾ [فُصِّلَت: 46]

Khaled Ibrahim Betala
“Amene achite chabwino, akudzichitira yekha; ndipo amene akuipitsa (m’zochita zake), machimo ake ali pa iye yekha. Mbuye wako sali wopondereza akapolo (Ake polanga wina ndi tchimo la wina)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek