×

Ndipo, ndithudi, Ife tikamuonetsera chifundo chathu atazunzika, ndithudi iye adzati: “Ichi ndi 41:50 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Fussilat ⮕ (41:50) ayat 50 in Chichewa

41:50 Surah Fussilat ayat 50 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 50 - فُصِّلَت - Page - Juz 25

﴿وَلَئِنۡ أَذَقۡنَٰهُ رَحۡمَةٗ مِّنَّا مِنۢ بَعۡدِ ضَرَّآءَ مَسَّتۡهُ لَيَقُولَنَّ هَٰذَا لِي وَمَآ أَظُنُّ ٱلسَّاعَةَ قَآئِمَةٗ وَلَئِن رُّجِعۡتُ إِلَىٰ رَبِّيٓ إِنَّ لِي عِندَهُۥ لَلۡحُسۡنَىٰۚ فَلَنُنَبِّئَنَّ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ بِمَا عَمِلُواْ وَلَنُذِيقَنَّهُم مِّنۡ عَذَابٍ غَلِيظٖ ﴾
[فُصِّلَت: 50]

Ndipo, ndithudi, Ife tikamuonetsera chifundo chathu atazunzika, ndithudi iye adzati: “Ichi ndi chifukwa cha nzeru zanga ndipo ine sindiganiza kuti ola lidzadza. Ndipo ngati ine ndibwerera kwa Ambuye wanga, ndithudi ine ndidzalandira zabwino kuchokera kwa Iye.” Ndithudi, Ife tidzawauza onse amene samakhulupirira zonse zimene adachita ndipo, ndithudi, Ife tidzawapatsa chilango chowawa kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولئن أذقناه رحمة منا من بعد ضراء مسته ليقولن هذا لي وما, باللغة نيانجا

﴿ولئن أذقناه رحمة منا من بعد ضراء مسته ليقولن هذا لي وما﴾ [فُصِّلَت: 50]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ndithu tikamulawitsa chisomo chochokera kwa Ife atapeza mavuto kwambiri amene adamkhudza, ndithu amanena, (monyada): “Izi nzangazanga. (Ndazipeza chifukwa cha khama langa ndi nzeru zanga). Ndipo za tsiku lachimaliziro sindikhulupirira kuti lilipo. Ndipo ngati nditabwezedwa kwa Mbuye wanga, ndiye kuti ine ndidzakhala nazo zabwino kwa Iye.” Choncho tidzawauza omwe adakanira zimene adachita, ndipo tidzawalawitsa chilango chokhwima (chosanjikana china pamwamba pa chinzake)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek