Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 51 - فُصِّلَت - Page - Juz 25
﴿وَإِذَآ أَنۡعَمۡنَا عَلَى ٱلۡإِنسَٰنِ أَعۡرَضَ وَنَـَٔا بِجَانِبِهِۦ وَإِذَا مَسَّهُ ٱلشَّرُّ فَذُو دُعَآءٍ عَرِيضٖ ﴾
[فُصِّلَت: 51]
﴿وإذا أنعمنا على الإنسان أعرض ونأى بجانبه وإذا مسه الشر فذو دعاء﴾ [فُصِّلَت: 51]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo munthu tikam’dalitsa (ndi chisomo Chathu), amanyoza ndi kudziika kutali (ndi chipembedzo Chathu). Koma vuto likam’khudza umuona uyo akuchulukitsa maduwa (mapemphero) |