Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 53 - فُصِّلَت - Page - Juz 25
﴿سَنُرِيهِمۡ ءَايَٰتِنَا فِي ٱلۡأٓفَاقِ وَفِيٓ أَنفُسِهِمۡ حَتَّىٰ يَتَبَيَّنَ لَهُمۡ أَنَّهُ ٱلۡحَقُّۗ أَوَلَمۡ يَكۡفِ بِرَبِّكَ أَنَّهُۥ عَلَىٰ كُلِّ شَيۡءٖ شَهِيدٌ ﴾
[فُصِّلَت: 53]
﴿سنريهم آياتنا في الآفاق وفي أنفسهم حتى يتبين لهم أنه الحق أو﴾ [فُصِّلَت: 53]
Khaled Ibrahim Betala “Posachedwa tiwaonetsa (awa okanira), zisonyezo Zathu (zosonyeza kuona kwa Qur’an ndi iwe) kumbali zonse, ndi mwa iwo eni kufikira zionekere kwa iwo kuti chimene wadza nachochi nchoona. Kodi Mbuye wako siwokwanira kuti Iye akuona chilichonse |