Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 54 - فُصِّلَت - Page - Juz 25
﴿أَلَآ إِنَّهُمۡ فِي مِرۡيَةٖ مِّن لِّقَآءِ رَبِّهِمۡۗ أَلَآ إِنَّهُۥ بِكُلِّ شَيۡءٖ مُّحِيطُۢ ﴾
[فُصِّلَت: 54]
﴿ألا إنهم في مرية من لقاء ربهم ألا إنه بكل شيء محيط﴾ [فُصِّلَت: 54]
Khaled Ibrahim Betala “Chenjerani! Ndithu awa ali m’chikaiko za kukumana ndi Mbuye wawo. Ndithu Iye (Mbuye wawo) wachizungulira chinthu chilichonse mkudziwa Kwake |