Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 52 - فُصِّلَت - Page - Juz 25
﴿قُلۡ أَرَءَيۡتُمۡ إِن كَانَ مِنۡ عِندِ ٱللَّهِ ثُمَّ كَفَرۡتُم بِهِۦ مَنۡ أَضَلُّ مِمَّنۡ هُوَ فِي شِقَاقِۭ بَعِيدٖ ﴾
[فُصِّلَت: 52]
﴿قل أرأيتم إن كان من عند الله ثم كفرتم به من أضل﴾ [فُصِّلَت: 52]
Khaled Ibrahim Betala “Nena (kwa iwo, iwe Mtumiki): “Tandiuzani ngati (Qur’aniyi) ilidi yochokera kwa Allah, kenako inu nkuikanira; (nanga zingakhale bwanji?) Kodi ndiyani wosokera kwambiri kuposa uyo amene ali mu mtsutso wakutali (ndi choona)?” |