Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shura ayat 34 - الشُّوري - Page - Juz 25
﴿أَوۡ يُوبِقۡهُنَّ بِمَا كَسَبُواْ وَيَعۡفُ عَن كَثِيرٖ ﴾
[الشُّوري: 34]
﴿أو يوبقهن بما كسبوا ويعف عن كثير﴾ [الشُّوري: 34]
Khaled Ibrahim Betala “Kapena akhoza kuziononga (potumiza mphepo yamkuntho) chifukwa cha machimo amene adawachita. Koma amakhululuka zambiri |