Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shura ayat 40 - الشُّوري - Page - Juz 25
﴿وَجَزَٰٓؤُاْ سَيِّئَةٖ سَيِّئَةٞ مِّثۡلُهَاۖ فَمَنۡ عَفَا وَأَصۡلَحَ فَأَجۡرُهُۥ عَلَى ٱللَّهِۚ إِنَّهُۥ لَا يُحِبُّ ٱلظَّٰلِمِينَ ﴾
[الشُّوري: 40]
﴿وجزاء سيئة سيئة مثلها فمن عفا وأصلح فأجره على الله إنه لا﴾ [الشُّوري: 40]
Khaled Ibrahim Betala “Malipiro a choipa ndi choipa chonga icho; (wochita choipa alipidwe choipa chonga chimene wachita). Koma amene wakhululukira wochita choipa (pomwe akhoza kubwezera), ndi kuyanjana naye (mdani wakeyo), malipiro ake ali kwa Allah; ndithu Allah sakonda ochitira anzawo mtopola |