Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 18 - الزُّخرُف - Page - Juz 25
﴿أَوَمَن يُنَشَّؤُاْ فِي ٱلۡحِلۡيَةِ وَهُوَ فِي ٱلۡخِصَامِ غَيۡرُ مُبِينٖ ﴾
[الزُّخرُف: 18]
﴿أو من ينشأ في الحلية وهو في الخصام غير مبين﴾ [الزُّخرُف: 18]
Khaled Ibrahim Betala “Ha! Kodi amene waleredwa monga chokongoletsa, potsutsana iye sangathe kunena momveka? (Ameneyo ndiye mwampatsa Allah; omwe ndi ana aakazi) |