×

Ndipo iwo amasandutsa angelo amene ali akapolo a Mulungu, kukhala akazi. Kodi 43:19 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zukhruf ⮕ (43:19) ayat 19 in Chichewa

43:19 Surah Az-Zukhruf ayat 19 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 19 - الزُّخرُف - Page - Juz 25

﴿وَجَعَلُواْ ٱلۡمَلَٰٓئِكَةَ ٱلَّذِينَ هُمۡ عِبَٰدُ ٱلرَّحۡمَٰنِ إِنَٰثًاۚ أَشَهِدُواْ خَلۡقَهُمۡۚ سَتُكۡتَبُ شَهَٰدَتُهُمۡ وَيُسۡـَٔلُونَ ﴾
[الزُّخرُف: 19]

Ndipo iwo amasandutsa angelo amene ali akapolo a Mulungu, kukhala akazi. Kodi iwo adaonerera chilengedwe chawo? Umboni wawo udzalembedwa ndipo iwo adzafunsidwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وجعلوا الملائكة الذين هم عباد الرحمن إناثا أشهدوا خلقهم ستكتب شهادتهم ويسألون, باللغة نيانجا

﴿وجعلوا الملائكة الذين هم عباد الرحمن إناثا أشهدوا خلقهم ستكتب شهادتهم ويسألون﴾ [الزُّخرُف: 19]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo angelo omwe ndi akapolo a (Allah) Wachifundo chambiri akuwatcha akazi. Kodi adaona kalengedwe kawo? Umboni wawo ulembedwa ndipo adzafunsidwa (pazimenezo)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek